Account Boosting

Kuphunzira kupanga boost ma accounts 

Ku phunziroli la account boosting timaphunzitsa njira zosiyanasiyana za zinthu zomwe tikuyenera kuchita kuti tizipeza ma likes komanso ma followers ku ma facebook accounts athu, ma TikTok accounts, ma instagram accounts komanso ma social media platforms otchuka pa dziko lonse lino.

UBWINO WAPHUNZIRO LA ACCOUNT BOOSTING

1. Imatithandiza kumapeza malikes komanso ma followers ochokera dziko lililonse lomwe tafuna 

2. Ndinjiranso imodzi yomwe titha kumapezera ndalama chifukwa mutha kumawapangira anthu ena ma account awo kut nawonso azipeza ma likes komanso ma followers a size yabho monga kupeza ma 1k, 2k komanso kuchepera apo.

Kuphunziro ili muzaphunzira mmene mungapezere ma followers komanso ma likes amtundu iliwonse omwe mungafune kuti muzipeza kapena kuti muzikhala nawo kuma social media accounts onse omwe tafuna.